Salimo 90:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti ife tatha chifukwa cha mkwiyo wanu,+Ndipo tasokonezeka chifukwa cha kupsa mtima kwanu.+