1 Mbiri 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kuwonjezera apo, Aisiraeli onse, mwamuna komanso mkazi, aliyense wa iwo anapatsidwa+ keke yozungulira, zipatso za kanjedza zouma zoumba pamodzi ndi mphesa zouma zoumba pamodzi.
3 Kuwonjezera apo, Aisiraeli onse, mwamuna komanso mkazi, aliyense wa iwo anapatsidwa+ keke yozungulira, zipatso za kanjedza zouma zoumba pamodzi ndi mphesa zouma zoumba pamodzi.