Deuteronomo 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 dziko la tirigu, balere, mphesa, nkhuyu ndi makangaza,*+ dziko la maolivi opangira mafuta ndiponso la uchi,+ Yesaya 36:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 kufikira ine nditabwera kudzakutengerani kudziko lofanana ndi dziko lanulo.+ Ndidzakutengerani kudziko la mbewu ndi la vinyo watsopano, dziko la mkate ndi minda ya mpesa.
8 dziko la tirigu, balere, mphesa, nkhuyu ndi makangaza,*+ dziko la maolivi opangira mafuta ndiponso la uchi,+
17 kufikira ine nditabwera kudzakutengerani kudziko lofanana ndi dziko lanulo.+ Ndidzakutengerani kudziko la mbewu ndi la vinyo watsopano, dziko la mkate ndi minda ya mpesa.