2 Mbiri 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chotero, Yehova anapulumutsa Hezekiya ndi anthu okhala ku Yerusalemu m’manja mwa Senakeribu mfumu ya Asuri+ komanso m’manja mwa ena onse, ndipo anawapatsa mpumulo kwa adani awo onse owazungulira.+
22 Chotero, Yehova anapulumutsa Hezekiya ndi anthu okhala ku Yerusalemu m’manja mwa Senakeribu mfumu ya Asuri+ komanso m’manja mwa ena onse, ndipo anawapatsa mpumulo kwa adani awo onse owazungulira.+