2 Mafumu 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho mukagwetse mzinda uliwonse wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri,+ mzinda uliwonse wabwino kwambiri,+ ndi mtengo uliwonse wabwino.+ Mukatseke akasupe onse amadzi, ndipo mukawononge malo alionse abwino mwa kuponyapo miyala.”
19 Choncho mukagwetse mzinda uliwonse wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri,+ mzinda uliwonse wabwino kwambiri,+ ndi mtengo uliwonse wabwino.+ Mukatseke akasupe onse amadzi, ndipo mukawononge malo alionse abwino mwa kuponyapo miyala.”