1 Mbiri 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Salumu anabereka Hilikiya,+ Hilikiya anabereka Azariya, 1 Mbiri 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ndi Azariya+ mwana wa Hilikiya. Hilikiya anali mwana wa Mesulamu, Mesulamu anali mwana wa Zadoki, Zadoki anali mwana wa Merayoti, ndipo Merayoti anali mwana wa Ahitubu. Ahitubu anali mtsogoleri wa nyumba ya Mulungu woona.
11 ndi Azariya+ mwana wa Hilikiya. Hilikiya anali mwana wa Mesulamu, Mesulamu anali mwana wa Zadoki, Zadoki anali mwana wa Merayoti, ndipo Merayoti anali mwana wa Ahitubu. Ahitubu anali mtsogoleri wa nyumba ya Mulungu woona.