2 Mbiri 34:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ine ndidzakugoneka pamodzi ndi makolo ako, ndipo ndithu udzaikidwa m’manda ako mu mtendere.+ Maso ako sadzaona tsoka+ lonse limene ndikulibweretsa pamalo ano ndi anthu ake.’”’”+ Anthuwo anabweretsa mawuwo kwa mfumuyo.
28 Ine ndidzakugoneka pamodzi ndi makolo ako, ndipo ndithu udzaikidwa m’manda ako mu mtendere.+ Maso ako sadzaona tsoka+ lonse limene ndikulibweretsa pamalo ano ndi anthu ake.’”’”+ Anthuwo anabweretsa mawuwo kwa mfumuyo.