Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 36:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo anabwera+ kudzam’manga ndi zomangira ziwiri zamkuwa n’kupita naye ku Babulo.+

  • Yeremiya 22:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Adzaikidwa m’manda ngati mmene amaikira bulu wamphongo.+ Adzamukoka kudutsa naye pazipata za Yerusalemu ndi kukamutaya kunja.’+

  • Yeremiya 36:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Choncho ponena za chilango chimene adzapatsa Yehoyakimu mfumu ya Yuda, Yehova wanena kuti, ‘Sipadzapezeka mwana wake aliyense wokhala pampando wachifumu wa Davide.+ Mtembo wake adzautaya kunja+ kumene udzakhala padzuwa lotentha masana ndipo usiku udzakhala kunja kozizira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena