Yeremiya 52:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ziwerengero za anthu amene Nebukadirezara anawatenga kupita nawo ku ukapolo ndi izi: m’chaka cha 7 cha ulamuliro wake, anatenga Ayuda 3,023.+
28 Ziwerengero za anthu amene Nebukadirezara anawatenga kupita nawo ku ukapolo ndi izi: m’chaka cha 7 cha ulamuliro wake, anatenga Ayuda 3,023.+