Mateyu 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo Yesu anamuyankha kuti: “Mayi iwe, chikhulupiriro chako ndi chachikulu. Zimene ukufuna zichitike kwa iwe.” Ndipo kuchokera mu ola limenelo mwana wake anachira.+ Yohane 11:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Yesu anati: “Kodi sindinakuuze kuti ngati ukhulupirira udzaona ulemerero wa Mulungu?”+
28 Pamenepo Yesu anamuyankha kuti: “Mayi iwe, chikhulupiriro chako ndi chachikulu. Zimene ukufuna zichitike kwa iwe.” Ndipo kuchokera mu ola limenelo mwana wake anachira.+