2 Mafumu 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ahabu atangomwalira,+ mfumu ya Mowabu inapandukira+ mfumu ya Isiraeli. 2 Mafumu 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Aedomu anapitirizabe kugalukira Yuda mpaka lero. Inalinso nthawi imeneyi pamene Libina+ anagalukira Yuda.
22 Koma Aedomu anapitirizabe kugalukira Yuda mpaka lero. Inalinso nthawi imeneyi pamene Libina+ anagalukira Yuda.