Luka 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mmodzi wa iwo ataona kuti wachiritsidwa, anabwerera, akutamanda Mulungu+ mokweza mawu.