2 Samueli 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Davide atamva zimenezi anamukwiyira kwambiri munthuyo,+ moti anauza Natani kuti: “Ndithu, pali Yehova Mulungu wamoyo,+ munthu wochita zimenezi ayenera kufa!+
5 Davide atamva zimenezi anamukwiyira kwambiri munthuyo,+ moti anauza Natani kuti: “Ndithu, pali Yehova Mulungu wamoyo,+ munthu wochita zimenezi ayenera kufa!+