2 Mafumu 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano magulu achifwamba a Asiriya+ anapita kudziko la Isiraeli komwe anakagwirako kamtsikana n’kupita nako kwawo.+ Kenako kamtsikanako kanayamba kutumikira mkazi wa Namani.
2 Tsopano magulu achifwamba a Asiriya+ anapita kudziko la Isiraeli komwe anakagwirako kamtsikana n’kupita nako kwawo.+ Kenako kamtsikanako kanayamba kutumikira mkazi wa Namani.