2 Mafumu 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako Elisa analowa m’nyumbamo ndipo anapeza mwana wakufayo atam’goneka pabedi lake lija.+