Mika 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwe mkazi wokhala ku Lakisi,+ mangirira galeta ku gulu la mahatchi.* Mzinda umenewu ndiwo unayambitsa tchimo la mwana wamkazi wa Ziyoni,+ pakuti kupanduka kwa Isiraeli kwapezeka mwa iwe.+
13 Iwe mkazi wokhala ku Lakisi,+ mangirira galeta ku gulu la mahatchi.* Mzinda umenewu ndiwo unayambitsa tchimo la mwana wamkazi wa Ziyoni,+ pakuti kupanduka kwa Isiraeli kwapezeka mwa iwe.+