1 Mafumu 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye atamva anati: “Agwireni amoyo, kaya abwerera mtendere kapena abwerera nkhondo.”+