1 Mafumu 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho mfumuyo inakambirana ndi anthu ena+ n’kupanga ana awiri a ng’ombe agolide.+ Itatero inauza anthuwo kuti: “N’zovuta kwambiri kwa inu kuti muzipita ku Yerusalemu. Nayu Mulungu wanu+ Aisiraeli inu, amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo.”+ Hoseya 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zimenezi zachokera ku Isiraeli.+ Mmisiri ndiye anapanga fano la mwana wa ng’ombe la ku Samariya.+ Fanolo si Mulungu woona, chifukwa lidzangokhala ngati nkhuni zowazawaza.+
28 Choncho mfumuyo inakambirana ndi anthu ena+ n’kupanga ana awiri a ng’ombe agolide.+ Itatero inauza anthuwo kuti: “N’zovuta kwambiri kwa inu kuti muzipita ku Yerusalemu. Nayu Mulungu wanu+ Aisiraeli inu, amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo.”+
6 Zimenezi zachokera ku Isiraeli.+ Mmisiri ndiye anapanga fano la mwana wa ng’ombe la ku Samariya.+ Fanolo si Mulungu woona, chifukwa lidzangokhala ngati nkhuni zowazawaza.+