Deuteronomo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mafuko a Rubeni+ ndi Gadi ndinawapatsa dera lochokera ku Giliyadi+ kukafika kuchigwa cha Arinoni, ndipo malire anali pakati pa chigwacho. Dera limeneli linakafikanso kuchigwa cha Yaboki, amene ndi malire a ana a Amoni.+
16 Mafuko a Rubeni+ ndi Gadi ndinawapatsa dera lochokera ku Giliyadi+ kukafika kuchigwa cha Arinoni, ndipo malire anali pakati pa chigwacho. Dera limeneli linakafikanso kuchigwa cha Yaboki, amene ndi malire a ana a Amoni.+