2 Mafumu 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 M’chaka cha 7 cha Yehu,+ Yehoasi+ anakhala mfumu ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 40. Mayi ake anali a ku Beere-seba ndipo dzina lawo linali Zibiya.
12 M’chaka cha 7 cha Yehu,+ Yehoasi+ anakhala mfumu ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 40. Mayi ake anali a ku Beere-seba ndipo dzina lawo linali Zibiya.