Miyambo 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mudzi umakondwera chifukwa cha makhalidwe abwino a anthu olungama,+ koma anthu oipa akawonongeka pamakhala mfuu yachisangalalo.+ Miyambo 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Olungama akachuluka, anthu amasangalala,+ koma aliyense woipa akayamba kulamulira, anthu amabuula.+
10 Mudzi umakondwera chifukwa cha makhalidwe abwino a anthu olungama,+ koma anthu oipa akawonongeka pamakhala mfuu yachisangalalo.+
2 Olungama akachuluka, anthu amasangalala,+ koma aliyense woipa akayamba kulamulira, anthu amabuula.+