2 Mafumu 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno ufumuwo utangokhazikika m’manja mwake, iye anayamba kupha+ atumiki ake amene anapha bambo ake, omwe anali mfumu.+
5 Ndiyeno ufumuwo utangokhazikika m’manja mwake, iye anayamba kupha+ atumiki ake amene anapha bambo ake, omwe anali mfumu.+