Chivumbulutso 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Masiku atatu ndi hafu+ aja atatha, mzimu wa moyo wochokera kwa Mulungu unalowa mwa mboni zija.+ Ndiyeno mbonizo zinaimirira, ndipo amene anali kuziona anagwidwa ndi mantha aakulu.
11 Masiku atatu ndi hafu+ aja atatha, mzimu wa moyo wochokera kwa Mulungu unalowa mwa mboni zija.+ Ndiyeno mbonizo zinaimirira, ndipo amene anali kuziona anagwidwa ndi mantha aakulu.