Ezekieli 47:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno anandiuza kuti: “Madzi awa akupita kuchigawo cha kum’mawa, ndipo adutsa ku Araba+ n’kukafika kunyanja.+ Madziwa akakafika kunyanjako,+ akachititsa madzi a m’nyanjamo kukhala abwino.
8 Ndiyeno anandiuza kuti: “Madzi awa akupita kuchigawo cha kum’mawa, ndipo adutsa ku Araba+ n’kukafika kunyanja.+ Madziwa akakafika kunyanjako,+ akachititsa madzi a m’nyanjamo kukhala abwino.