Yona 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Yehova anayamba kulankhula ndi Yona+ mwana wa Amitai, kuti: Mateyu 12:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Poyankha iye anawauza kuti: “M’badwo woipa ndi wachigololo+ ukufunitsitsabe chizindikiro. Sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse koma chizindikiro cha mneneri Yona chokha.+
39 Poyankha iye anawauza kuti: “M’badwo woipa ndi wachigololo+ ukufunitsitsabe chizindikiro. Sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse koma chizindikiro cha mneneri Yona chokha.+