1 Mbiri 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa ana a Kohati panali Uriyeli+ mtsogoleri wawo ndi abale ake okwanira 120.