Genesis 36:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana a Reueli anali awa: Nahati, Zera, Shama ndi Miza.+ Amenewa ndiwo anali ana a Basemati+ mkazi wa Esau.
13 Ana a Reueli anali awa: Nahati, Zera, Shama ndi Miza.+ Amenewa ndiwo anali ana a Basemati+ mkazi wa Esau.