Genesis 36:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ana a Lotani anali Hori ndi Hemamu, ndipo Lotani anali ndi mlongo wake dzina lake Timina.+