1 Samueli 14:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Tsopano Sauli analimbitsa ufumu wake mu Isiraeli+ ndipo anamenya nkhondo ndi adani ake onse om’zungulira. Iye anamenyana ndi Mowabu,+ ana a Amoni,+ Edomu,+ mafumu a Zoba+ ndi Afilisiti.+ Kulikonse kumene anali kutembenukira anali kuwalanga.+
47 Tsopano Sauli analimbitsa ufumu wake mu Isiraeli+ ndipo anamenya nkhondo ndi adani ake onse om’zungulira. Iye anamenyana ndi Mowabu,+ ana a Amoni,+ Edomu,+ mafumu a Zoba+ ndi Afilisiti.+ Kulikonse kumene anali kutembenukira anali kuwalanga.+