2 Samueli 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Hanuni anatenga atumiki a Davide aja ndi kuwameta ndevu zonse za mbali imodzi,+ kenako anadula zovala zawo pakati moti zinalekeza m’matako, n’kuwauza kuti azipita.+
4 Pamenepo Hanuni anatenga atumiki a Davide aja ndi kuwameta ndevu zonse za mbali imodzi,+ kenako anadula zovala zawo pakati moti zinalekeza m’matako, n’kuwauza kuti azipita.+