1 Samueli 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Isiraeli yense anamva anthu akukamba kuti: “Sauli wakantha mudzi wa asilikali a Afilisiti, ndipo tsopano Isiraeli wakhala chinthu chonunkha+ kwa Afilisiti.” Choncho anasonkhanitsa anthu onse pamodzi kuti atsatire Sauli ku Giligala.+
4 Isiraeli yense anamva anthu akukamba kuti: “Sauli wakantha mudzi wa asilikali a Afilisiti, ndipo tsopano Isiraeli wakhala chinthu chonunkha+ kwa Afilisiti.” Choncho anasonkhanitsa anthu onse pamodzi kuti atsatire Sauli ku Giligala.+