2 Samueli 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo ana a Amoni ataona kuti Asiriya athawa, nawonso anathawa pamaso pa Abisai ndi kubwerera kwawo.+ Kenako Yowabu anasiya kutsatira ana a Amoni ndi kubwerera ku Yerusalemu.+
14 Pamenepo ana a Amoni ataona kuti Asiriya athawa, nawonso anathawa pamaso pa Abisai ndi kubwerera kwawo.+ Kenako Yowabu anasiya kutsatira ana a Amoni ndi kubwerera ku Yerusalemu.+