2 Samueli 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Davide atamva zimenezi, nthawi yomweyo anasonkhanitsa Aisiraeli onse ndi kuwoloka Yorodano kupita ku Helamu. Ndiyeno Asiriya anafola kuti akumane ndi Davide ndi kuyamba kumenyana naye.+
17 Davide atamva zimenezi, nthawi yomweyo anasonkhanitsa Aisiraeli onse ndi kuwoloka Yorodano kupita ku Helamu. Ndiyeno Asiriya anafola kuti akumane ndi Davide ndi kuyamba kumenyana naye.+