1 Mafumu 6:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kenako anamanga khoma la miyala yosema lotalika mizere itatu+ kuzungulira bwalo lamkati,+ ndipo anawonjezeranso mzere umodzi wa matabwa a mkungudza.
36 Kenako anamanga khoma la miyala yosema lotalika mizere itatu+ kuzungulira bwalo lamkati,+ ndipo anawonjezeranso mzere umodzi wa matabwa a mkungudza.