Numeri 26:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Koma Nadabu ndi Abihu anafa chifukwa chofukiza moto wosaloleka pamaso pa Yehova.+