Luka 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’masiku a Herode,*+ mfumu ya Yudeya, kunali wansembe wina wotchedwa Zekariya wa m’gulu la ansembe lotchedwa Abiya.+ Iyeyu anali ndi mkazi wochokera mwa ana aakazi a Aroni,+ dzina lake Elizabeti.
5 M’masiku a Herode,*+ mfumu ya Yudeya, kunali wansembe wina wotchedwa Zekariya wa m’gulu la ansembe lotchedwa Abiya.+ Iyeyu anali ndi mkazi wochokera mwa ana aakazi a Aroni,+ dzina lake Elizabeti.