1 Mbiri 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ana a Gerisomu, mtsogoleri wawo anali Sebueli.+ 1 Mbiri 26:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ndipo Sebueli+ mwana wa Gerisomu mwana wa Mose, anali mtsogoleri panyumba zosungiramo katundu.