1 Mbiri 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ana a Yuda anali Perezi,+ Hezironi,+ Karami,+ Hura,+ ndi Sobala.+