Ezekieli 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwe unali kuchita malonda ndi Yavani,+ Tubala+ ndi Meseke.+ Unali kuwapatsa katundu wako wogulitsa pomusinthanitsa ndi anthu+ komanso zinthu zamkuwa.
13 Iwe unali kuchita malonda ndi Yavani,+ Tubala+ ndi Meseke.+ Unali kuwapatsa katundu wako wogulitsa pomusinthanitsa ndi anthu+ komanso zinthu zamkuwa.