1 Mbiri 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo Davide ndi Aisiraeli onse anali kusangalala kwadzaoneni+ pamaso pa Mulungu woona. Anali kuimba nyimbo+ ndi azeze,+ zoimbira za zingwe,+ maseche,+ zinganga ndi malipenga.+
8 Ndipo Davide ndi Aisiraeli onse anali kusangalala kwadzaoneni+ pamaso pa Mulungu woona. Anali kuimba nyimbo+ ndi azeze,+ zoimbira za zingwe,+ maseche,+ zinganga ndi malipenga.+