1 Mbiri 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Kohati+ analipo anayi. Panali Amuramu, Izara,+ Heburoni+ ndi Uziyeli.+