Rute 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Panali munthu wina wolemera kwambiri+ yemwe anali wachibale+ wa mwamuna wake wa Naomi. Dzina lake anali Boazi,+ wa kubanja la Elimeleki. Mateyu 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Salimoni anabereka Boazi, ndipo mayi ake anali Rahabi.+Boazi anabereka Obedi, ndipo mayi ake anali Rute.+Obedi anabereka Jese.+
2 Panali munthu wina wolemera kwambiri+ yemwe anali wachibale+ wa mwamuna wake wa Naomi. Dzina lake anali Boazi,+ wa kubanja la Elimeleki.
5 Salimoni anabereka Boazi, ndipo mayi ake anali Rahabi.+Boazi anabereka Obedi, ndipo mayi ake anali Rute.+Obedi anabereka Jese.+