Mlaliki 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komanso, phindu la dziko lapansi ndi la munthu aliyense,+ chifukwa ngakhale mfumu imadalira kuti munda wake ulimidwe, kuti ipindule ndi zokolola za kumundako.+
9 Komanso, phindu la dziko lapansi ndi la munthu aliyense,+ chifukwa ngakhale mfumu imadalira kuti munda wake ulimidwe, kuti ipindule ndi zokolola za kumundako.+