1 Samueli 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Davide anakantha dzikolo ndipo sanasiye mwamuna kapena mkazi aliyense ali wamoyo.+ Iye anatenga nkhosa, ng’ombe, abulu, ngamila ndi zovala. Atatero anabwerera ndi kupita kwa Akisi.
9 Davide anakantha dzikolo ndipo sanasiye mwamuna kapena mkazi aliyense ali wamoyo.+ Iye anatenga nkhosa, ng’ombe, abulu, ngamila ndi zovala. Atatero anabwerera ndi kupita kwa Akisi.