1 Mbiri 27:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Azimaveti mwana wa Adieli anali kuyang’anira chuma cha mfumu.+ Yonatani mwana wa Uziya anali kuyang’anira chuma chosungidwa m’madera apafupi,+ m’mizinda,+ m’midzi ndi m’nyumba zosanja. 1 Mbiri 27:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Sitirai wa ku Sharoni+ anali kuyang’anira zoweta zimene anali kudyetsera ku Sharoni. Safati mwana wa Adilai anali kuyang’anira zoweta zimene zinali kuzigwa.
25 Azimaveti mwana wa Adieli anali kuyang’anira chuma cha mfumu.+ Yonatani mwana wa Uziya anali kuyang’anira chuma chosungidwa m’madera apafupi,+ m’mizinda,+ m’midzi ndi m’nyumba zosanja.
29 Sitirai wa ku Sharoni+ anali kuyang’anira zoweta zimene anali kudyetsera ku Sharoni. Safati mwana wa Adilai anali kuyang’anira zoweta zimene zinali kuzigwa.