1 Mbiri 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Davide anasonkhanitsa zitsulo zambirimbiri zopangira misomali ya zitseko za pazipata komanso zopangira zida zopanira zinthu. Anasonkhanitsanso mkuwa wambirimbiri wosatheka kuuyeza kulemera kwake.+
3 Ndiyeno Davide anasonkhanitsa zitsulo zambirimbiri zopangira misomali ya zitseko za pazipata komanso zopangira zida zopanira zinthu. Anasonkhanitsanso mkuwa wambirimbiri wosatheka kuuyeza kulemera kwake.+