1 Mafumu 7:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 M’kupita kwa nthawi, Solomo anapanga ziwiya zonse za panyumba ya Yehova, za paguwa lansembe+ lagolide, ndi za patebulo+ limene ankaikapo mkate wachionetsero.
48 M’kupita kwa nthawi, Solomo anapanga ziwiya zonse za panyumba ya Yehova, za paguwa lansembe+ lagolide, ndi za patebulo+ limene ankaikapo mkate wachionetsero.