-
1 Mbiri 22:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Taona, pa nthawi ya masautso anga+ ndasonkhanitsa golide womangira nyumba ya Yehova wokwanira matalente* 100,000,+ ndi siliva wokwanira matalente 1,000,000. Koma n’zosatheka kuyeza kulemera kwa mkuwa+ ndi zitsulo+ chifukwa n’zochuluka kwambiri. Ndakonzanso matabwa ndi miyala, koma udzawonjezerapo zina.
-