1 Mafumu 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumuyo inapitiriza kuti: “Adalitsike Yehova+ Mulungu wa Isiraeli, amene analankhula ndi pakamwa pake kwa Davide+ bambo anga, ndipo ndi dzanja lake wakwaniritsa zimene ananena,+ zakuti,
15 Mfumuyo inapitiriza kuti: “Adalitsike Yehova+ Mulungu wa Isiraeli, amene analankhula ndi pakamwa pake kwa Davide+ bambo anga, ndipo ndi dzanja lake wakwaniritsa zimene ananena,+ zakuti,