2 Samueli 13:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma Abisalomu anathawa ndi kupita kwa Talimai,+ mfumu ya dziko la Gesuri,+ amene anali mwana wamwamuna wa Amihudi. Davide anali kulira+ tsiku ndi tsiku chifukwa cha imfa ya Aminoni mwana wake.
37 Koma Abisalomu anathawa ndi kupita kwa Talimai,+ mfumu ya dziko la Gesuri,+ amene anali mwana wamwamuna wa Amihudi. Davide anali kulira+ tsiku ndi tsiku chifukwa cha imfa ya Aminoni mwana wake.